Ezekieli 23:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Asilikaliwo adzawagenda ndi miyala+ nʼkuwapha ndi malupanga. Adzaphanso ana awo aamuna ndi aakazi+ ndipo adzawotcha nyumba zawo.+
47 Asilikaliwo adzawagenda ndi miyala+ nʼkuwapha ndi malupanga. Adzaphanso ana awo aamuna ndi aakazi+ ndipo adzawotcha nyumba zawo.+