Ezekieli 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nena mwambi wokhudza anthu opanduka. Unene zokhudza anthu amenewa kuti: ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ika mphika* pamoto ndipo uthiremo madzi.+
3 Nena mwambi wokhudza anthu opanduka. Unene zokhudza anthu amenewa kuti: ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ika mphika* pamoto ndipo uthiremo madzi.+