Ezekieli 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa magazi amene mzindawo wakhetsa ali mkati mwake.+ Wathira magaziwo pathanthwe lopanda chilichonse. Mzindawo sunathire magaziwo pansi kuti uwakwirire ndi dothi.+
7 Chifukwa magazi amene mzindawo wakhetsa ali mkati mwake.+ Wathira magaziwo pathanthwe lopanda chilichonse. Mzindawo sunathire magaziwo pansi kuti uwakwirire ndi dothi.+