Ezekieli 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine Yehova ndanena ndipo zidzachitikadi. Ndidzachitapo kanthu mosazengereza, popanda kumva chisoni kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako komanso zochita zako,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
14 Ine Yehova ndanena ndipo zidzachitikadi. Ndidzachitapo kanthu mosazengereza, popanda kumva chisoni kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako komanso zochita zako,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”