Ezekieli 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Iwe mwana wa munthu, ine ndichititsa kuti mkazi wako afe mwadzidzidzi.+ Koma iwe usamve chisoni,* kulira kapena kugwetsa misozi. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:16 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 21
16 “Iwe mwana wa munthu, ine ndichititsa kuti mkazi wako afe mwadzidzidzi.+ Koma iwe usamve chisoni,* kulira kapena kugwetsa misozi.