Ezekieli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ulire mosatulutsa mawu ndipo usachite miyambo yamaliro.+ Uvale nduwira kumutu+ ndipo uvale nsapato zako.+ Usaphimbe ndevu zako zapamlomo+ ndipo usadye chakudya chimene anthu angakupatse.”+
17 Ulire mosatulutsa mawu ndipo usachite miyambo yamaliro.+ Uvale nduwira kumutu+ ndipo uvale nsapato zako.+ Usaphimbe ndevu zako zapamlomo+ ndipo usadye chakudya chimene anthu angakupatse.”+