Ezekieli 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako nʼkulankhula ndi munthu amene wapulumukayo ndipo sudzakhalanso chete.+ Iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo, ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.” Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:27 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, ptsa. 13-1412/1/2003, tsa. 299/15/1988, tsa. 21
27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako nʼkulankhula ndi munthu amene wapulumukayo ndipo sudzakhalanso chete.+ Iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo, ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”