-
Ezekieli 25:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Uuze Aamoniwo kuti, ‘Imvani mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu munanena kuti ‘Eyaa! Zakhala bwino.’ Munanena zimenezi malo anga opatulika atadetsedwa, dziko la Isiraeli litasanduka bwinja komanso nyumba ya Yuda itatengedwa kupita ku ukapolo.
-