Ezekieli 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mzinda wa Raba+ ndidzausandutsa malo odyetserako ngamila, ndipo dziko la Aamoni ndidzalisandutsa malo opumilako ziweto ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”
5 Mzinda wa Raba+ ndidzausandutsa malo odyetserako ngamila, ndipo dziko la Aamoni ndidzalisandutsa malo opumilako ziweto ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”