Ezekieli 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Ine ndidzabwezera Edomu pogwiritsa ntchito anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndikuwabwezera,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’
14 ‘Ine ndidzabwezera Edomu pogwiritsa ntchito anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndikuwabwezera,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’