Ezekieli 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mayikowo adzagwetsa mipanda ya Turo komanso kugumula nsanja zake.+ Ine ndidzapala dothi lake nʼkumusandutsa thanthwe losalala lopanda kanthu. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:4 Mawu a Mulungu, ptsa. 120-122
4 Mayikowo adzagwetsa mipanda ya Turo komanso kugumula nsanja zake.+ Ine ndidzapala dothi lake nʼkumusandutsa thanthwe losalala lopanda kanthu.