Ezekieli 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu amʼmidzi yake imene ili* kunja kwa mzindawo adzaphedwa ndi lupanga ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’
6 ‘Anthu amʼmidzi yake imene ili* kunja kwa mzindawo adzaphedwa ndi lupanga ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’