-
Ezekieli 26:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Anthu omwe akukhala mʼmidzi yako imene ili kunja kwa mzindawu adzawapha ndi lupanga. Iye adzamanga mpanda womenyerapo nkhondo komanso malo okwera omenyerapo nkhondo kuti amenyane nawe ndipo adzakuukira ndi chishango chachikulu.
-