Ezekieli 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘Ndidzathetsa phokoso la nyimbo zako ndipo phokoso la azeze ako silidzamvekanso.+