Ezekieli 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mzinda wa Turo kuti: ‘Kodi zilumba sizidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kugwa kwako, kubuula kwa anthu amene avulazidwa koopsa* komanso chifukwa cha kuphedwa kwa anthu ako ambiri?+
15 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mzinda wa Turo kuti: ‘Kodi zilumba sizidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kugwa kwako, kubuula kwa anthu amene avulazidwa koopsa* komanso chifukwa cha kuphedwa kwa anthu ako ambiri?+