Ezekieli 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndikadzakuwononga ngati mizinda imene simukukhala anthu, ndikadzakubweretsera madzi ambiri, ndipo madzi amphamvu akadzakumiza,+
19 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndikadzakuwononga ngati mizinda imene simukukhala anthu, ndikadzakubweretsera madzi ambiri, ndipo madzi amphamvu akadzakumiza,+