Ezekieli 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amuna a ku Perisiya, ku Ludi ndi ku Puti+ anali mʼgulu lako lankhondo, anali mʼgulu la asilikali ako. Iwo ankapachika zishango ndi zipewa zawo pamakoma ako ndipo anakubweretsera ulemerero.
10 Amuna a ku Perisiya, ku Ludi ndi ku Puti+ anali mʼgulu lako lankhondo, anali mʼgulu la asilikali ako. Iwo ankapachika zishango ndi zipewa zawo pamakoma ako ndipo anakubweretsera ulemerero.