Ezekieli 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tarisi+ ankachita nawe malonda chifukwa unali ndi chuma chochuluka.+ Anakupatsa siliva, chitsulo, tini ndi mtovu kuti atenge katundu wako.+
12 Tarisi+ ankachita nawe malonda chifukwa unali ndi chuma chochuluka.+ Anakupatsa siliva, chitsulo, tini ndi mtovu kuti atenge katundu wako.+