-
Ezekieli 27:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Edomu ankachita nawe malonda chifukwa chakuti unali ndi katundu wochuluka. Anakupatsa miyala ya nofeki, ubweya wa nkhosa wapepo, nsalu zopeta zamitundu yosiyanasiyana, nsalu zabwino kwambiri, miyala yamtengo wapatali ya korali ndi ya rube posinthanitsa ndi katundu wako.
-