Ezekieli 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Vedani ndi Yavani akudera la Uzali anakupatsa ziwiya zachitsulo, mitengo ya kasiya* ndi mabango onunkhira posinthanitsa ndi katundu wako.
19 Vedani ndi Yavani akudera la Uzali anakupatsa ziwiya zachitsulo, mitengo ya kasiya* ndi mabango onunkhira posinthanitsa ndi katundu wako.