Ezekieli 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Katundu wako atabwera kuchokera pakatikati pa nyanja, unasangalatsa anthu ambiri.+ Chuma chako chochuluka komanso malonda ako zinalemeretsa mafumu apadziko lapansi.+
33 Katundu wako atabwera kuchokera pakatikati pa nyanja, unasangalatsa anthu ambiri.+ Chuma chako chochuluka komanso malonda ako zinalemeretsa mafumu apadziko lapansi.+