Ezekieli 27:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu onse amene akukhala mʼzilumba adzakuyangʼanitsitsa modabwa,+Ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zidzaoneka zankhawa.
35 Anthu onse amene akukhala mʼzilumba adzakuyangʼanitsitsa modabwa,+Ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zidzaoneka zankhawa.