Ezekieli 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Luso lako pa malonda linakubweretsera chuma chochuluka,+Ndipo mtima wako unayamba kudzikuza chifukwa cha chuma chakocho.”’
5 Luso lako pa malonda linakubweretsera chuma chochuluka,+Ndipo mtima wako unayamba kudzikuza chifukwa cha chuma chakocho.”’