-
Ezekieli 28:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 ‘Udzafa ngati anthu osadulidwa ndipo anthu amʼmayiko ena ndi amene adzakuphe,
Ine ndanena,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-