-
Ezekieli 28:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo. Uuze mfumuyo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:
-