-
Ezekieli 28:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Choncho ndidzakuchotsa mʼphiri la Mulungu nʼkukuponya kunja monga wodetsedwa ndipo ndidzakuwononga.+
Iwe kerubi amene umagwira ntchito yoteteza, ndidzakuchotsa pakati pa miyala yamoto.
-