Ezekieli 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtima wako unadzikweza chifukwa cha kukongola kwako.+ Unawononga nzeru zako chifukwa cha ulemerero wako waukulu.+ Ndidzakuponyera kudziko lapansi,+ Ndipo mafumu azidzakuyangʼanitsitsa.
17 Mtima wako unadzikweza chifukwa cha kukongola kwako.+ Unawononga nzeru zako chifukwa cha ulemerero wako waukulu.+ Ndidzakuponyera kudziko lapansi,+ Ndipo mafumu azidzakuyangʼanitsitsa.