-
Ezekieli 28:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:
“Iwe Sidoni, ine ndikupatsa chilango ndipo ndidzalemekezedwa pakati pako.
Ndikadzapereka chiweruzo kwa iwe komanso ndikadzayeretsedwa kudzera mwa iwe, anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.
-