Ezekieli 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zikadzatero, nyumba ya Isiraeli sidzazunguliridwanso ndi anthu amene amawanyoza, omwe ali ngati zitsamba zobaya komanso minga zaululu.+ Ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’
24 Zikadzatero, nyumba ya Isiraeli sidzazunguliridwanso ndi anthu amene amawanyoza, omwe ali ngati zitsamba zobaya komanso minga zaululu.+ Ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’