25 ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikadzasonkhanitsanso pamodzi nyumba ya Isiraeli kuchokera kwa anthu a mitundu ina kumene anabalalikira,+ ndidzayeretsedwa pakati pawo pamaso pa mitundu ina ya anthu.+ Ndipo anthuwo adzakhala mʼdziko+ limene ndinapatsa mtumiki wanga Yakobo.+