Ezekieli 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Adzakhala mʼdzikolo motetezeka+ ndipo adzamanga nyumba komanso kulima minda ya mpesa.+ Iwo azidzakhala motetezeka ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene amawanyoza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’”
26 Adzakhala mʼdzikolo motetezeka+ ndipo adzamanga nyumba komanso kulima minda ya mpesa.+ Iwo azidzakhala motetezeka ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene amawanyoza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’”