Ezekieli 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti: ‘Anthu amene akuthandiza Iguputo nawonso adzaphedwa,Ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga mʼdzikolo kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
6 Yehova wanena kuti: ‘Anthu amene akuthandiza Iguputo nawonso adzaphedwa,Ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga mʼdzikolo kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.