-
Ezekieli 30:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndikadzayatsa moto mu Iguputo komanso ndikadzaphwanya onse amene akuthandizana nawo, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.
-