-
Ezekieli 30:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Pa tsikulo, ndidzatumiza amithenga pasitima zapamadzi kuti akaopseze Itiyopiya yemwe ndi wodzidalira. Itiyopiya adzachita mantha kwambiri pa tsiku limene Iguputo adzawonongedwe, chifukwa tsikulo lidzafika ndithu.’
-