Ezekieli 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumuyo ndi asilikali ake, omwe ndi ankhanza kwambiri pa mayiko onse,+ adzabweretsedwa kuti adzawononge dzikolo. Iwo adzasolola malupanga awo nʼkuukira Iguputo ndipo adzadzaza dzikolo ndi anthu ophedwa.+
11 Mfumuyo ndi asilikali ake, omwe ndi ankhanza kwambiri pa mayiko onse,+ adzabweretsedwa kuti adzawononge dzikolo. Iwo adzasolola malupanga awo nʼkuukira Iguputo ndipo adzadzaza dzikolo ndi anthu ophedwa.+