Ezekieli 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzayatsa moto mu Iguputo. Sini adzachita mantha kwambiri ndipo adani adzagumula mpanda wa No nʼkulowa mumzindamo. Adani adzaukira mzinda wa Nofi* dzuwa likuswa mtengo.
16 Ndidzayatsa moto mu Iguputo. Sini adzachita mantha kwambiri ndipo adani adzagumula mpanda wa No nʼkulowa mumzindamo. Adani adzaukira mzinda wa Nofi* dzuwa likuswa mtengo.