Ezekieli 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mumzinda wa Tahapanesi mudzagwa mdima masana ndikadzathyola magoli a Iguputo kumeneko.+ Mphamvu zimene amanyadira zidzatha.+ Mitambo idzamuphimba ndipo anthu amʼmatauni ake adzatengedwa kupita ku ukapolo.+
18 Mumzinda wa Tahapanesi mudzagwa mdima masana ndikadzathyola magoli a Iguputo kumeneko.+ Mphamvu zimene amanyadira zidzatha.+ Mitambo idzamuphimba ndipo anthu amʼmatauni ake adzatengedwa kupita ku ukapolo.+