Ezekieli 30:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ine ndidzabalalitsira Aiguputo ku mitundu ina ya anthu nʼkuwamwaza mʼmayiko ena+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
26 Ine ndidzabalalitsira Aiguputo ku mitundu ina ya anthu nʼkuwamwaza mʼmayiko ena+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”