Ezekieli 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, uza Farao mfumu ya Iguputo ndi magulu a anthu amene amamutsatira+ kuti,‘Kodi ndi ndani amene ali wamphamvu ngati iwe?
2 “Iwe mwana wa munthu, uza Farao mfumu ya Iguputo ndi magulu a anthu amene amamutsatira+ kuti,‘Kodi ndi ndani amene ali wamphamvu ngati iwe?