-
Ezekieli 31:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Iwe uli ngati Msuri, mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,
Wa nthambi zokongola ngati ziyangoyango za masamba ambiri, mtengo wautali kwambiri,
Umene nsonga yake inafika mʼmitambo.
-