12 Anthu amʼmayiko ena, mitundu ya anthu yankhanza kwambiri, adzadula mtengowo ndipo adzausiya mʼmapiri. Masamba ake adzagwera mʼzigwa zonse ndipo nthambi zake zidzathyoka nʼkugwera mʼmitsinje yonse yamʼdzikolo.+ Mitundu yonse ya anthu apadziko lapansi idzachoka mumthunzi wake nʼkuusiya.