-
Ezekieli 31:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Phokoso la kugwa kwake likadzamveka, ndidzachititsa kuti mitundu ya anthu injenjemere ndikamadzatsitsira mtengowo ku Manda* pamodzi ndi onse amene akutsikira kudzenje.* Ndipo mitengo yonse ya mu Edeni+ komanso mitengo yonse yabwino kwambiri ya ku Lebanoni imene ili pamadzi ambiri, idzatonthozedwa pansi pa nthaka.
-