Ezekieli 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndikadzakuzimitsa, ndidzaphimba kumwamba nʼkuchititsa mdima nyenyezi zake. Dzuwa ndidzaliphimba ndi mitambo,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:7 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, tsa. 17
7 Ndikadzakuzimitsa, ndidzaphimba kumwamba nʼkuchititsa mdima nyenyezi zake. Dzuwa ndidzaliphimba ndi mitambo,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.+