-
Ezekieli 32:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndidzachititsa mantha anthu ambiri a mitundu ina,
Ndipo mafumu awo adzanjenjemera ndi mantha chifukwa cha iwe ndikadzawaloza ndi lupanga langa.
Iwo azidzanjenjemera mosalekeza chifukwa choopa kufa,
Pa tsiku limene udzaphedwe.’
-