Ezekieli 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Lupanga la mfumu ya Babulo lidzakuukira.+