Ezekieli 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Iwe mwana wa munthu, lirira gulu la anthu onse a ku Iguputo ndipo utsitsire dzikolo kumanda. Utsitsire kumanda dzikolo ndi ana aakazi a mitundu yamphamvu limodzi ndi amene akutsikira kudzenje.*
18 “Iwe mwana wa munthu, lirira gulu la anthu onse a ku Iguputo ndipo utsitsire dzikolo kumanda. Utsitsire kumanda dzikolo ndi ana aakazi a mitundu yamphamvu limodzi ndi amene akutsikira kudzenje.*