-
Ezekieli 32:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Manda a Asuri ali pakatikati pa dzenje ndipo gulu lake lonse lazungulira manda akewo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga chifukwa anachititsa kuti anthu amene akukhala mʼdziko la anthu amoyo azikhala mwamantha.
-