Ezekieli 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Farao adzaona zinthu zonsezi ndipo mtima wake udzakhala mʼmalo chifukwa cha zonse zimene zinachitikira gulu la anthu amene ankamutsatira.+ Farao ndi asilikali ake onse adzaphedwa ndi lupanga,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
31 Farao adzaona zinthu zonsezi ndipo mtima wake udzakhala mʼmalo chifukwa cha zonse zimene zinachitikira gulu la anthu amene ankamutsatira.+ Farao ndi asilikali ake onse adzaphedwa ndi lupanga,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.