Ezekieli 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi anthu a mtundu wako+ ndipo uwauze kuti,‘Tiyerekeze kuti ndabweretsa lupanga mʼdziko,+ ndiyeno anthu onse amʼdzikolo asankha munthu kuti akhale mlonda wawo,
2 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi anthu a mtundu wako+ ndipo uwauze kuti,‘Tiyerekeze kuti ndabweretsa lupanga mʼdziko,+ ndiyeno anthu onse amʼdzikolo asankha munthu kuti akhale mlonda wawo,