Ezekieli 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati mlondayo waona lupanga likubwera, koma iye osaliza lipenga,+ anthu osamva chenjezo lililonse, lupangalo nʼkufika ndi kupha munthu, munthuyo adzafa chifukwa cha zolakwa zake, koma mlondayo ndidzamuimba mlandu chifukwa cha imfa ya munthuyo.’*+
6 Ngati mlondayo waona lupanga likubwera, koma iye osaliza lipenga,+ anthu osamva chenjezo lililonse, lupangalo nʼkufika ndi kupha munthu, munthuyo adzafa chifukwa cha zolakwa zake, koma mlondayo ndidzamuimba mlandu chifukwa cha imfa ya munthuyo.’*+